21 Ndipo adzabala mwana wamwamuna, ndipo udzamucha dzina lace Yesu; pakuti Iyeyo adzapulumutsa anthu ace ku macimo ao.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 1
Onani Mateyu 1:21 nkhani