Mateyu 10:1 BL92

1 Ndipo pamene Iye anadziitanira ophunzira ace khumi ndi awiri, anapatsa iwo mphamvu pa mizimu yoipa, yakuiturutsa, ndi yakuciza nthenda iri yonse ndi zofoka zonse.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 10

Onani Mateyu 10:1 nkhani