14 Ndipo yemwe sadzakulandirani inu, kapena kusamva mau anu, pamene mulikuturuka m'nyumbayo, kapena m'mudzimo, sansani pfumbi m'mapazi anu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:14 nkhani