Mateyu 10:22 BL92

22 Ndipo adzada inu anthu onse cifukwa ca dzina langa; koma iye wakupirira kufikira cimariziro, iyeyu adzapulumutsidwa.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 10

Onani Mateyu 10:22 nkhani