37 5 Iye wakukonda atate wace, kapena amace koposa Ine, sayenera Ine, ndipo iye wakukonda mwana wace wamwamuna, kapena wamkazi koposa Ine, sayenera Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:37 nkhani