5 Awa amene, khumi ndi awiriwa, Yesu anawatumiza, nawalangiza ndi kuti,Musapite ku njira ya kwa anthu akunja, ndi m'mudzi wa Asamariya musamalowamo:
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:5 nkhani