16 Koma ndidzafanizira ndi ciani obadwa awa a makono? Ali ofanana ndi ana akukhala m'mabwalo a malonda, amene alikuitana anzao,
Werengani mutu wathunthu Mateyu 11
Onani Mateyu 11:16 nkhani