29 Senzani gori langa, ndipo phunzirani kwa Ine; cifukwa ndiri wofatsa ndi wodzicepetsa mtima: ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 11
Onani Mateyu 11:29 nkhani