Mateyu 11:5 BL92

5 akhungu alandira kuona kwao, Ndi opunduka miyendo ayenda, akhate akonzedwa, indi ogontha akumva, ndi akufa aukitsidwa, ndi kwa aumphawi ulalikidwa uthenga wabwino.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 11

Onani Mateyu 11:5 nkhani