9 Koma munaturukiranji? Kukaona mneneri kodi? Indetu, ndinena kwa inu, wakuposa mneneri.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 11
Onani Mateyu 11:9 nkhani