13 Pomwepo ananena Iye kwa munthuyo, Tansa dzanja Lako. Ndipo iye analitansa, ndipo linabwezedwa lamoyo longa linzace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:13 nkhani