Mateyu 12:36 BL92

36 Ndipo ndinena kwa inu, kuti mau onse opanda pace, amene anthu adzalankhula, adzawawerengera mlandu wace tsiku la kuweruza.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 12

Onani Mateyu 12:36 nkhani