Mateyu 13:17 BL92

17 Pakuti indetu ndinena kwa inu, kuti aneneri ambiri ndi anthu olungama analakalaka kupenya zimene muziona, koma sanaziona; ndi kumva zimene muzimva, koma sanazimva.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:17 nkhani