Mateyu 13:19 BL92

19 Munthu ali yense wakumva mau a Ufumu, osawadziwitsai, woipayo angodza, nakwatula cofesedwaco mumtima mwace. Uyo ndiye wofesedwa m'mbali mwa njira.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:19 nkhani