Mateyu 13:2 BL92

2 Ndipo makamu ambiri a anthu anasonkhanira kwa Iye, kotero kuti Iye analowa m'ngalawa, nakhala pansi, ndipo khamu lonse linaima pamtunda.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:2 nkhani