Mateyu 13:41 BL92

41 Mwana wa munthu adzatuma angelo ace, ndipo iwo adzasonkhanitsa pamodzi, ndi kucotsa mu Ufumu wace zokhumudwitsa zonse, ndi anthu akucita kusayeruzika,

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:41 nkhani