Mateyu 14:2 BL92

2 nanena kwa anyamata ace, U yo ndiye Yohane Mbatizi; anauka kwa akufa; ndipo cifukwa ca ici zamphamvuzi zilimbalimba mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 14

Onani Mateyu 14:2 nkhani