Mateyu 14:23 BL92

23 Ndipo pamene Iye anawauza makamuwo, anakwera m'phiri pa yekha, kukapemphera: ndipo pamene panali madzulo, Iye anakhala kumeneko yekha.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 14

Onani Mateyu 14:23 nkhani