Mateyu 14:26 BL92

26 Koma m'mene ophunzirawo anamuona Iye, alikuyenda pamadzi, ananthunthumira, nati, ndi mzukwa! Ndipo anapfuula ndi mantha.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 14

Onani Mateyu 14:26 nkhani