31 Ndipo pomwepo Yesu anatansa dzanja lace, namgwira iye, nanena naye, Iwe wokhulupirira pang'ono, wakayikiranji mtima?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 14
Onani Mateyu 14:31 nkhani