Mateyu 14:6 BL92

6 Koma pakufika tsiku la kubadwa kwace kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiya anabvina pakati pao, namkondweretsa Herode.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 14

Onani Mateyu 14:6 nkhani