8 Ndipo iye, atampangira amace, anati, Ndipatseni ine kuno m'mbizi mutu wa Yohane Mbatizi. Ndipo mfumuyo anagwidwa ndi cisoni;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 14
Onani Mateyu 14:8 nkhani