14 Kawalekeni iwo, ali atsogoleri akhungu. Ndipo ngati wakhungu amtsogolera wakhungu, onse awiri adzagwa m'mbuna.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:14 nkhani