34 Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Muli nayo mikate ingati? Ndipo iwo anati, Isanu ndi iwiri, ndi tinsomba pang'ono.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:34 nkhani