36 natenga mikateyo isanu ndi iwiri ndi nsombazo; nayamika Mulungu, nanyema, napatsa kwa ophunzira, ndi ophunzira kwa anthu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:36 nkhani