12 Pomwepo anadziwitsa kuti sanawauza kupewa cotupitsa ca mikate, koma ciphunzitso ca Afarisi ndi Asaduki.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:12 nkhani