Mateyu 16:14 BL92

14 Ndipo iwo anati, Ena ati, Yohane Mbatizi; koma ena, Eliya; ndipo enanso Yeremiya, kapena mmodzi wa aneneri.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 16

Onani Mateyu 16:14 nkhani