17 Ndipo Yesu anayankha iye, nati, Ndiwe wodala, Simoni Bar-Yona: pakuti thupi ndi mwazi sizinakuululira ici, koma Atate wanga wa Kumwamba.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:17 nkhani