27 Pakuti Mwana wa munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wace, pamodzi ndi angelo ace; ndipo pomwepo Iye adzabwezera kwa anthu onse monga macitidwe ao.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:27 nkhani