15 Ambuye, citirani mwana wanga cifundo; cifukwa adwala khunyu, kuzunzika koipa: pakuti amagwa kawiri kawiri pamoto, ndi kawiri kawiri m'madzi.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 17
Onani Mateyu 17:15 nkhani