Mateyu 17:17 BL92

17 Ndipo Yesu anayankha nati, Ha, obadwa osakhulupirira ndi amphulupulu, ndidzakhala ndi inu nthawi yanji? ndidzalekerera inu nthawi yanji? mudze naye kwa Ine kuno.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 17

Onani Mateyu 17:17 nkhani