2 ndipo Iye anasandulika pamaso pao; ndipo nkhope yace inawala monga dzuwa, ndi zobvala zace zinakhala zoyera mbu monga kuwala.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 17
Onani Mateyu 17:2 nkhani