26 Ndipo m'mene iye anati, Kwa akunja, Yesu ananena kwa iye, Cifukwa cace anawo ali aufulu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 17
Onani Mateyu 17:26 nkhani