9 Ndipo pamene anali kutsika paphiri, Yesu anawalangiza iwo kuti, Musakauze munthu coonekaco, kufikira Mwana wa munthu adadzauka kwa akufa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 17
Onani Mateyu 17:9 nkhani