16 Koma ngati samvera, onjeza kutenga ndi iwe wina mmodzi kapena awiri, kuti atsimikizidwe mau onse pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:16 nkhani