19 Ndiponso ndinena kwa inu kuti ngati awiri ainu abvomerezana pansi pano cinthu ciri conse akacipempha, Atate wanga wa Kumwamba adzawacitira.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:19 nkhani