21 Pamenepo Petro anadza, nati kwa Iye, Ambuye, mbale wanga adzandilakwira kangati, ndipo ine ndidzamkhululukira iye? kufikira kasanu ndi kawiri kodi?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:21 nkhani