25 Koma popeza iye anasowa kanthu kombwezera, mbuye wace analamulira kuti iye agulitsidwe, ndi mkazi wace ndi ana ace omwe, ndi zonse ali nazo, kuti akabwezedwe mangawawo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:25 nkhani