28 Koma kapolo uyu, poturuka anapeza wina wa akapolo anzace yemwe anamkongola iye marupiya atheka makumi khumi, namgwira, namkanyanga pakhosi, nati, Bwezera cija unacikongola.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:28 nkhani