Mateyu 18:9 BL92

9 Ndipo ngati diso lako likukhumudwitsa, ulikolowole, nulitaye: nkwabwino kuti ulowe m'moyo ndi diso limodzi koposa kuponyedwa m'gehena wamoto, uli ndi maso awiri.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 18

Onani Mateyu 18:9 nkhani