17 Ndipo Iye anati kwa iye, Undifunsiranji za cinthu cabwino? alipo Mmodzi ndiye wabwino: koma ngati ufuna kulowa m'moyo, sunga malamulo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 19
Onani Mateyu 19:17 nkhani