Mateyu 19:21 BL92

21 Yesu ananena naye, Ngati ufuna kukhala wangwiro, pita, kagulitse zomwe uli nazo, nupatse aumphawi, ndipo udzakhaia ndi cuma Kumwamba; ndipo ukadze kuno, unditsate.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 19

Onani Mateyu 19:21 nkhani