23 Ndipo Yesu anati kwa ophunzira ace, Indetu ndinena kwa inu, kuti munthu mwini cuma adzalowa mobvutika mu Ufumu wa Kumwamba.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 19
Onani Mateyu 19:23 nkhani