27 Pomwepo Petro anayankha, nati kwa Iye, Onani, ife tinasiya zonse ndi kutsata Inu; nanga tsono tidzakhala ndi ciani?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 19
Onani Mateyu 19:27 nkhani