3 Ndipo Afarisi anadza kwa Iye, namuyesa, nanena, Kodi nkuloledwa kuti munthu acotse mkazi wace pa cifukwa ciri conse?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 19
Onani Mateyu 19:3 nkhani