12 Ndipo iwo, pocenjezedwa m'kulota kuti asabwerere kwa Herode, anacoka kupita ku dziko lao pa njira yina.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 2
Onani Mateyu 2:12 nkhani