18 Mau anamveka m'Rama,Maliro ndi kucema kwambiri;Rakele wolira ana ace,Wosafuna kusangalatsidwa,Cifukwa palibe iwo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 2
Onani Mateyu 2:18 nkhani