20 nati, Tauka, nutenge kamwana ndi amace, nupite ku dziko la Israyeli: cifukwa anafa uja wofuna moyo wace wa kamwanako.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 2
Onani Mateyu 2:20 nkhani