9 Ndipo iwo, m'mene anamva mfumu, anamuka; ndipo onani, nyenyezi ija anaiona kum'mawa, inawatsogolera iwo, kufikira inadza niima pamwamba pomwe panali kamwanako.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 2
Onani Mateyu 2:9 nkhani