Mateyu 20:19 BL92

19 nadzampereka kwa anthu akunja kuti amnyoze ndi kumkwapula, ndi kumpacika; ndipo Iye adzaukitsidwa tsiku lacitatu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 20

Onani Mateyu 20:19 nkhani